×

Ndipo adalenga dzuwa ndi mwezi, zimene zimayenda mokhazikika m’misewu yawo kuti muzigwiritsa 14:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:33) ayat 33 in Chichewa

14:33 Surah Ibrahim ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 33 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿وَسَخَّرَ لَكُمُ ٱلشَّمۡسَ وَٱلۡقَمَرَ دَآئِبَيۡنِۖ وَسَخَّرَ لَكُمُ ٱلَّيۡلَ وَٱلنَّهَارَ ﴾
[إبراهِيم: 33]

Ndipo adalenga dzuwa ndi mwezi, zimene zimayenda mokhazikika m’misewu yawo kuti muzigwiritsa ntchito. Ndipo adalenga usiku ndi usana kuti muziugwiritsa ntchito

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وسخر لكم الشمس والقمر دائبين وسخر لكم الليل والنهار, باللغة نيانجا

﴿وسخر لكم الشمس والقمر دائبين وسخر لكم الليل والنهار﴾ [إبراهِيم: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Adakufewetseraninso dzuwa ndi mwezi, mopitilira (nthawi zonse). Ndiponso adakufewetserani usiku ndi usana
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek