×

Ndipo Iye adakupatsani zonse zimene mudamupempha ndipo ngati inu muwerenga zokoma za 14:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:34) ayat 34 in Chichewa

14:34 Surah Ibrahim ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 34 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿وَءَاتَىٰكُم مِّن كُلِّ مَا سَأَلۡتُمُوهُۚ وَإِن تَعُدُّواْ نِعۡمَتَ ٱللَّهِ لَا تُحۡصُوهَآۗ إِنَّ ٱلۡإِنسَٰنَ لَظَلُومٞ كَفَّارٞ ﴾
[إبراهِيم: 34]

Ndipo Iye adakupatsani zonse zimene mudamupempha ndipo ngati inu muwerenga zokoma za Mulungu inu simungathe kuziwerenga zonse. Zoonadi munthu ndi wosayamika ndi wosakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وآتاكم من كل ما سألتموه وإن تعدوا نعمة الله لا تحصوها إن, باللغة نيانجا

﴿وآتاكم من كل ما سألتموه وإن تعدوا نعمة الله لا تحصوها إن﴾ [إبراهِيم: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo wakupatsani mu zonse zomwe mwampempha (ndi zimene simudam’pemphe). Ngati mutayesa kuwerenga madalitso a Allah, simungathe kuwawerenga. Ndithu munthu ngwachinyengo chachikulu, ngosathokoza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek