Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 52 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿إِذۡ دَخَلُواْ عَلَيۡهِ فَقَالُواْ سَلَٰمٗا قَالَ إِنَّا مِنكُمۡ وَجِلُونَ ﴾
[الحِجر: 52]
﴿إذ دخلوا عليه فقالوا سلاما قال إنا منكم وجلون﴾ [الحِجر: 52]
Khaled Ibrahim Betala “Pamene adalowa kwa iye ndikunena: “Salaman (Mtendere!)” (Iyenso adawayankha: “Mtendere ukhalenso pa inu.” Ndipo Pamene adaona kuti akana chakudya) Adati: “Ndithu ife tikukuopani.” |