Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 71 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿قَالَ هَٰٓؤُلَآءِ بَنَاتِيٓ إِن كُنتُمۡ فَٰعِلِينَ ﴾
[الحِجر: 71]
﴿قال هؤلاء بناتي إن كنتم فاعلين﴾ [الحِجر: 71]
Khaled Ibrahim Betala “Iye adati: “Awa (akazi onsewa ali ngati) ana anga. Ngati inu ndinu ochita (chimene chalamulidwa, akwatireni; musachite zauve ndi alendowa).” |