Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 1 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿أَتَىٰٓ أَمۡرُ ٱللَّهِ فَلَا تَسۡتَعۡجِلُوهُۚ سُبۡحَٰنَهُۥ وَتَعَٰلَىٰ عَمَّا يُشۡرِكُونَ ﴾
[النَّحل: 1]
﴿أتى أمر الله فلا تستعجلوه سبحانه وتعالى عما يشركون﴾ [النَّحل: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Lamulo la Allah lidzafika, (ndithu) choncho, musalifulumizitse; (ndipo khulupirirani kuti Iye ndi Allah) Woyera Wopatukana ndi mbiri zopunguka, ndipo watukuka ku zomwe akumphatikiza nazo |