×

Iyeamatsitsaangelondimawuakeamalamulokwaakapolo ake amene wawafuna ndikuwauza kuti muwachenjeze iwo kuti, “Kulibe Mulungu wina 16:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:2) ayat 2 in Chichewa

16:2 Surah An-Nahl ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 2 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿يُنَزِّلُ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةَ بِٱلرُّوحِ مِنۡ أَمۡرِهِۦ عَلَىٰ مَن يَشَآءُ مِنۡ عِبَادِهِۦٓ أَنۡ أَنذِرُوٓاْ أَنَّهُۥ لَآ إِلَٰهَ إِلَّآ أَنَا۠ فَٱتَّقُونِ ﴾
[النَّحل: 2]

Iyeamatsitsaangelondimawuakeamalamulokwaakapolo ake amene wawafuna ndikuwauza kuti muwachenjeze iwo kuti, “Kulibe Mulungu wina koma Ine ndekha. Kotero ndiopeni Ine.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ينـزل الملائكة بالروح من أمره على من يشاء من عباده أن أنذروا, باللغة نيانجا

﴿ينـزل الملائكة بالروح من أمره على من يشاء من عباده أن أنذروا﴾ [النَّحل: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Amatumiza angelo pansi pamodzi ndi chivumbulutso mwa lamulo Lake (Allah), kwa omwe wawafuna mwa akapolo Ake (powauza) kuti: “Achenjezeni (anthu zakuti): ‘Palibe wopembedzedwa mwachoonadi koma Ine ndekha, choncho ndiopeni.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek