×

Ndipo anthu opembedza mafano amati, “Mulungu akadafuna, ife kapena makolo athu, sitikadapembedza 16:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:35) ayat 35 in Chichewa

16:35 Surah An-Nahl ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 35 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ أَشۡرَكُواْ لَوۡ شَآءَ ٱللَّهُ مَا عَبَدۡنَا مِن دُونِهِۦ مِن شَيۡءٖ نَّحۡنُ وَلَآ ءَابَآؤُنَا وَلَا حَرَّمۡنَا مِن دُونِهِۦ مِن شَيۡءٖۚ كَذَٰلِكَ فَعَلَ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِهِمۡۚ فَهَلۡ عَلَى ٱلرُّسُلِ إِلَّا ٱلۡبَلَٰغُ ٱلۡمُبِينُ ﴾
[النَّحل: 35]

Ndipo anthu opembedza mafano amati, “Mulungu akadafuna, ife kapena makolo athu, sitikadapembedza milungu ina yoonjezera pa Mulungu weniweni ayi ndiponso ife sitikadaletsa china chilichonse opanda chilolezo chake.” Mmenemo ndimo adachitira anthu amene adalipo kale iwo asanadze. Kodi Atumwi adapatsidwa china kupatula kupereka Uthenga momveka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الذين أشركوا لو شاء الله ما عبدنا من دونه من شيء, باللغة نيانجا

﴿وقال الذين أشركوا لو شاء الله ما عبدنا من دونه من شيء﴾ [النَّحل: 35]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek