Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 47 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿أَوۡ يَأۡخُذَهُمۡ عَلَىٰ تَخَوُّفٖ فَإِنَّ رَبَّكُمۡ لَرَءُوفٞ رَّحِيمٌ ﴾
[النَّحل: 47]
﴿أو يأخذهم على تخوف فإن ربكم لرءوف رحيم﴾ [النَّحل: 47]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena kuwalanga uku ali ndi mantha oyembekezera chilango (pakulanga m’modzim’modzi kufikira onse atatha)? Ndithu Mbuye wanu Ngodekha Ngwachisoni chosatha |