Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 46 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿أَوۡ يَأۡخُذَهُمۡ فِي تَقَلُّبِهِمۡ فَمَا هُم بِمُعۡجِزِينَ ﴾
[النَّحل: 46]
﴿أو يأخذهم في تقلبهم فما هم بمعجزين﴾ [النَّحل: 46]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena (Allah) kuwalanga mkuyenda kwawo kwa uku ndi uko? Pomwe iwo sangathe kumulepheretsa Allah kuchita chomwe wafuna pa iwo |