×

Ndipo zokoma zonse zimene mumalandira zimachokera kwa Mulungu. Ndipo pamene mavuto akupezani, 16:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:53) ayat 53 in Chichewa

16:53 Surah An-Nahl ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 53 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَمَا بِكُم مِّن نِّعۡمَةٖ فَمِنَ ٱللَّهِۖ ثُمَّ إِذَا مَسَّكُمُ ٱلضُّرُّ فَإِلَيۡهِ تَجۡـَٔرُونَ ﴾
[النَّحل: 53]

Ndipo zokoma zonse zimene mumalandira zimachokera kwa Mulungu. Ndipo pamene mavuto akupezani, inu mumapempha chithandizo kwa Iye

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما بكم من نعمة فمن الله ثم إذا مسكم الضر فإليه تجأرون, باللغة نيانجا

﴿وما بكم من نعمة فمن الله ثم إذا مسكم الضر فإليه تجأرون﴾ [النَّحل: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mtendere wonse umene muli nawo udachokera kwa Allah (koma inu simuthokoza), ndipo masautso akakukhudzani Iye ndi amene mumamulilira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek