×

Nena, “Ngati mukadakhala ndi nkhokwe za chifundo cha Ambuye wanga, ndithudi, inu 17:100 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:100) ayat 100 in Chichewa

17:100 Surah Al-Isra’ ayat 100 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 100 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قُل لَّوۡ أَنتُمۡ تَمۡلِكُونَ خَزَآئِنَ رَحۡمَةِ رَبِّيٓ إِذٗا لَّأَمۡسَكۡتُمۡ خَشۡيَةَ ٱلۡإِنفَاقِۚ وَكَانَ ٱلۡإِنسَٰنُ قَتُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 100]

Nena, “Ngati mukadakhala ndi nkhokwe za chifundo cha Ambuye wanga, ndithudi, inu mukanazibisa poopa kuti zingathe.” Ndithudi munthu ndi waumbombo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لو أنتم تملكون خزائن رحمة ربي إذا لأمسكتم خشية الإنفاق وكان, باللغة نيانجا

﴿قل لو أنتم تملكون خزائن رحمة ربي إذا لأمسكتم خشية الإنفاق وكان﴾ [الإسرَاء: 100]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena (kwa opembedza mafano): “Mukadakhala kuti muli nazo nkhokwe za chifundo cha Mbuye wanga, mukadachita umbombo (posagawira ena) kuopa umphawi. Ndipo munthu ali ndi khalidwe loumira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek