×

Nena, “Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu, amene sanabale mwana wamwamuna ndipo alibe 17:111 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:111) ayat 111 in Chichewa

17:111 Surah Al-Isra’ ayat 111 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 111 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَقُلِ ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِ ٱلَّذِي لَمۡ يَتَّخِذۡ وَلَدٗا وَلَمۡ يَكُن لَّهُۥ شَرِيكٞ فِي ٱلۡمُلۡكِ وَلَمۡ يَكُن لَّهُۥ وَلِيّٞ مِّنَ ٱلذُّلِّۖ وَكَبِّرۡهُ تَكۡبِيرَۢا ﴾
[الإسرَاء: 111]

Nena, “Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu, amene sanabale mwana wamwamuna ndipo alibe mnzake womuthandiza mu Ufumu wake, ndipo Iye siwopanda mphamvu kuti angakhale ndi womuthandiza. Motero mulemekezeni Iye ndi ulemu woyenera Iye yekha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقل الحمد لله الذي لم يتخذ ولدا ولم يكن له شريك في, باللغة نيانجا

﴿وقل الحمد لله الذي لم يتخذ ولدا ولم يكن له شريك في﴾ [الإسرَاء: 111]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo nena: “Kutamandidwa kwabwino nkwa Allah, yemwe saadadzipangire mwana, ndipo alibe m’phatikizi mu ufumu (Wake); ndipo alibe mthandizi (womthandiza) mkufooka; ndipo mkuzeni, kumkuza kwakukulu!”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek