×

Ndipo musachiyandikire chuma cha mwana wamasiye kupatula ngati muli ndi cholinga chochisamala 17:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:34) ayat 34 in Chichewa

17:34 Surah Al-Isra’ ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 34 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَلَا تَقۡرَبُواْ مَالَ ٱلۡيَتِيمِ إِلَّا بِٱلَّتِي هِيَ أَحۡسَنُ حَتَّىٰ يَبۡلُغَ أَشُدَّهُۥۚ وَأَوۡفُواْ بِٱلۡعَهۡدِۖ إِنَّ ٱلۡعَهۡدَ كَانَ مَسۡـُٔولٗا ﴾
[الإسرَاء: 34]

Ndipo musachiyandikire chuma cha mwana wamasiye kupatula ngati muli ndi cholinga chochisamala mpaka pamene mwini wake adzafike pa msinkhu woti akhoza kuchisamalira yekha. Ndipo kwaniritsani lonjezo lililonse. Ndithudi! mudzafunsidwa za lonjezoli

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تقربوا مال اليتيم إلا بالتي هي أحسن حتى يبلغ أشده وأوفوا, باللغة نيانجا

﴿ولا تقربوا مال اليتيم إلا بالتي هي أحسن حتى يبلغ أشده وأوفوا﴾ [الإسرَاء: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo musachiyandikire chuma cha wamasiye (pochidya mosayenera) koma pokhapokha m’njira yomwe ili yabwino, kufikira atakula, (apo tsono apatsidwe chumacho); ndipo kwaniritsani lonjezo, popeza lonjezo lidzafunsidwa (tsiku la Qiyâma)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek