×

Ndipo musaphe wina aliyense amene Mulungu waletsa pokhapokha ngati pali chifukwa chololedwa. 17:33 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:33) ayat 33 in Chichewa

17:33 Surah Al-Isra’ ayat 33 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 33 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَلَا تَقۡتُلُواْ ٱلنَّفۡسَ ٱلَّتِي حَرَّمَ ٱللَّهُ إِلَّا بِٱلۡحَقِّۗ وَمَن قُتِلَ مَظۡلُومٗا فَقَدۡ جَعَلۡنَا لِوَلِيِّهِۦ سُلۡطَٰنٗا فَلَا يُسۡرِف فِّي ٱلۡقَتۡلِۖ إِنَّهُۥ كَانَ مَنصُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 33]

Ndipo musaphe wina aliyense amene Mulungu waletsa pokhapokha ngati pali chifukwa chololedwa. Ndipo aliyense amene waphedwa mopanda chilungamo, Ife tamupatsa m’bale wake mphamvu zobwezera kapena kukhululuka pa imfa yake. Koma m’bale wakeyo asapyole muyeso pa kubwezeraku. Ndithudi iye ndi wotetezedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تقتلوا النفس التي حرم الله إلا بالحق ومن قتل مظلوما فقد, باللغة نيانجا

﴿ولا تقتلوا النفس التي حرم الله إلا بالحق ومن قتل مظلوما فقد﴾ [الإسرَاء: 33]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo musaphe munthu amene Allah waletsa (kumupha) koma mwachoonadi (poweruza oweruza zakuphedwa ngati utam’gwera mulandu woyenera kuphedwa). Ndipo amene waphedwa mopanda chilungamo, tapereka mphamvu kwa mlowammalo wake (wa wophedwayo atafuna angamuphenso kapena kumsiya ndikulandirapo dipo); koma asapyole malire mukuphako. Ndithu iye ngothandizidwa ndi Shariya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek