×

Ndipo kwaniritsani muyeso pamene muyesa zinthu ndipo yesani mwachilungamo polinga zinthu pa 17:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:35) ayat 35 in Chichewa

17:35 Surah Al-Isra’ ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 35 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَأَوۡفُواْ ٱلۡكَيۡلَ إِذَا كِلۡتُمۡ وَزِنُواْ بِٱلۡقِسۡطَاسِ ٱلۡمُسۡتَقِيمِۚ ذَٰلِكَ خَيۡرٞ وَأَحۡسَنُ تَأۡوِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 35]

Ndipo kwaniritsani muyeso pamene muyesa zinthu ndipo yesani mwachilungamo polinga zinthu pa sikelo. Zimenezo ndizo zabwino ndipo ndi mapeto abwino kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأوفوا الكيل إذا كلتم وزنوا بالقسطاس المستقيم ذلك خير وأحسن تأويلا, باللغة نيانجا

﴿وأوفوا الكيل إذا كلتم وزنوا بالقسطاس المستقيم ذلك خير وأحسن تأويلا﴾ [الإسرَاء: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kwaniritsani mlingo pamene mulinga, ndipo yesani ndi sikelo zabwino, zimenezo ndi zabwino (kwa inu) ndiponso mathero (ake) ngabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek