×

Ndipo musatsatire zinthu zimene simuzidziwa. Ndithudi kumvera kapena kuyang’ana kapenanso kuganizira kwa 17:36 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:36) ayat 36 in Chichewa

17:36 Surah Al-Isra’ ayat 36 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 36 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَلَا تَقۡفُ مَا لَيۡسَ لَكَ بِهِۦ عِلۡمٌۚ إِنَّ ٱلسَّمۡعَ وَٱلۡبَصَرَ وَٱلۡفُؤَادَ كُلُّ أُوْلَٰٓئِكَ كَانَ عَنۡهُ مَسۡـُٔولٗا ﴾
[الإسرَاء: 36]

Ndipo musatsatire zinthu zimene simuzidziwa. Ndithudi kumvera kapena kuyang’ana kapenanso kuganizira kwa mumtima mwa munthu kudzafufuzidwa pa tsiku lachiweruzo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تقف ما ليس لك به علم إن السمع والبصر والفؤاد كل, باللغة نيانجا

﴿ولا تقف ما ليس لك به علم إن السمع والبصر والفؤاد كل﴾ [الإسرَاء: 36]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo usazitsate (pongoziyankhulayankhula kapena kuzichita) zomwe sukuzidziwa; ndithu makutu, maso ndi mtima zonsezo zidzafunsidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek