×

Ambuye wako amadziwa kwambiri zonse zimene zili kumwamba ndi padziko lapansi ndipo, 17:55 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:55) ayat 55 in Chichewa

17:55 Surah Al-Isra’ ayat 55 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 55 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَرَبُّكَ أَعۡلَمُ بِمَن فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۗ وَلَقَدۡ فَضَّلۡنَا بَعۡضَ ٱلنَّبِيِّـۧنَ عَلَىٰ بَعۡضٖۖ وَءَاتَيۡنَا دَاوُۥدَ زَبُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 55]

Ambuye wako amadziwa kwambiri zonse zimene zili kumwamba ndi padziko lapansi ndipo, ndithudi, Ife tidalemekeza Aneneri ena kuposa anzawo ndipo kwa Davide, Ife tidamupatsa Buku la Masalimo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وربك أعلم بمن في السموات والأرض ولقد فضلنا بعض النبيين على بعض, باللغة نيانجا

﴿وربك أعلم بمن في السموات والأرض ولقد فضلنا بعض النبيين على بعض﴾ [الإسرَاء: 55]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo Mbuye wako akuwadziwa bwino onse ali kumwamba ndi pansi, ndithu tawapatsa ulemelero wambiri aneneri ena kuposa ena. Ndipo Daud tidampatsa Zaburi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek