×

Nena, “Aitaneni onse amene mumadzinyengeza nawo mowonjezera pa Iye. Iwo alibe mphamvu 17:56 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:56) ayat 56 in Chichewa

17:56 Surah Al-Isra’ ayat 56 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 56 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قُلِ ٱدۡعُواْ ٱلَّذِينَ زَعَمۡتُم مِّن دُونِهِۦ فَلَا يَمۡلِكُونَ كَشۡفَ ٱلضُّرِّ عَنكُمۡ وَلَا تَحۡوِيلًا ﴾
[الإسرَاء: 56]

Nena, “Aitaneni onse amene mumadzinyengeza nawo mowonjezera pa Iye. Iwo alibe mphamvu zochotsa mavuto anu kapena kuwasintha ndi kupatsa munthu wina.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل ادعوا الذين زعمتم من دونه فلا يملكون كشف الضر عنكم ولا, باللغة نيانجا

﴿قل ادعوا الذين زعمتم من دونه فلا يملكون كشف الضر عنكم ولا﴾ [الإسرَاء: 56]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Aitaneni amene mukuwatcha kuti ndi milungu kusiya Iye (Allah) kuti akuchotsereni masautso, sadzatha kukuchotserani vuto lililonse ngakhale kulisintha (kuti likhale chabwino).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek