×

Iwo amene amawapembedza nawonso amafunafuna njira yodziyandikiritsira kwa Ambuye wawo, kuti ndani 17:57 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:57) ayat 57 in Chichewa

17:57 Surah Al-Isra’ ayat 57 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 57 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿أُوْلَٰٓئِكَ ٱلَّذِينَ يَدۡعُونَ يَبۡتَغُونَ إِلَىٰ رَبِّهِمُ ٱلۡوَسِيلَةَ أَيُّهُمۡ أَقۡرَبُ وَيَرۡجُونَ رَحۡمَتَهُۥ وَيَخَافُونَ عَذَابَهُۥٓۚ إِنَّ عَذَابَ رَبِّكَ كَانَ مَحۡذُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 57]

Iwo amene amawapembedza nawonso amafunafuna njira yodziyandikiritsira kwa Ambuye wawo, kuti ndani amene angakhale pafupi kwambiri ndi Mulungu ndipo amafunafuna mtendere wa Mulungu ndikuopa chilango chake. Ndithudi chilango cha Ambuye wako ndi chofuna kuopedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أولئك الذين يدعون يبتغون إلى ربهم الوسيلة أيهم أقرب ويرجون رحمته ويخافون, باللغة نيانجا

﴿أولئك الذين يدعون يبتغون إلى ربهم الوسيلة أيهم أقرب ويرجون رحمته ويخافون﴾ [الإسرَاء: 57]

Khaled Ibrahim Betala
“Iwo amene akuwapempha (naonso) akufunafuna njira yoziyandikitsira kwa Mbuye wawo (ngakhale) omwe ali pafupi mwa iwo (ndi Allah, monga angelo); naonso akuyembekezera chifundo chake ndi kuopa chilango chake; ndithu chilango cha Mbuye wako, nchoopedwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek