×

Ndipo palibe mzinda umene Ife sitingauononge kapena kuulanga ndi chilango choopsa tsiku 17:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:58) ayat 58 in Chichewa

17:58 Surah Al-Isra’ ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 58 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَإِن مِّن قَرۡيَةٍ إِلَّا نَحۡنُ مُهۡلِكُوهَا قَبۡلَ يَوۡمِ ٱلۡقِيَٰمَةِ أَوۡ مُعَذِّبُوهَا عَذَابٗا شَدِيدٗاۚ كَانَ ذَٰلِكَ فِي ٱلۡكِتَٰبِ مَسۡطُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 58]

Ndipo palibe mzinda umene Ife sitingauononge kapena kuulanga ndi chilango choopsa tsiku lachiweruzo lisanadze. Izi zidalembedwa m’Buku

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن من قرية إلا نحن مهلكوها قبل يوم القيامة أو معذبوها عذابا, باللغة نيانجا

﴿وإن من قرية إلا نحن مهلكوها قبل يوم القيامة أو معذبوها عذابا﴾ [الإسرَاء: 58]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo sipadzapezeka mudzi uliwonse koma Ife tidzauphwasula tsiku la Qiyâma lisanadze, kapena tidzaulanga ndi chilango chaukali (ngati uli woyenerana ndi zimenezo). Izi zidalembedwa m’buku
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek