×

Iye adati, “Mukumuona! Uyu ndiye amene mwamulemekeza kuposa ine ndipo ngati inu 17:62 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:62) ayat 62 in Chichewa

17:62 Surah Al-Isra’ ayat 62 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 62 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قَالَ أَرَءَيۡتَكَ هَٰذَا ٱلَّذِي كَرَّمۡتَ عَلَيَّ لَئِنۡ أَخَّرۡتَنِ إِلَىٰ يَوۡمِ ٱلۡقِيَٰمَةِ لَأَحۡتَنِكَنَّ ذُرِّيَّتَهُۥٓ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 62]

Iye adati, “Mukumuona! Uyu ndiye amene mwamulemekeza kuposa ine ndipo ngati inu mundisunga ndi moyo mpaka patsiku louka kwa akufa, ine ndidzawasokoneza ana ake kupatula ochepa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال أرأيتك هذا الذي كرمت علي لئن أخرتني إلى يوم القيامة لأحتنكن, باللغة نيانجا

﴿قال أرأيتك هذا الذي كرمت علي لئن أخرتني إلى يوم القيامة لأحتنكن﴾ [الإسرَاء: 62]

Khaled Ibrahim Betala
“Adatinso (kwa Allah): “Kodi mukuona uyu amene mwampatsa ulemelero kuposa ine? Ngati mundipatsa nthawi mpaka tsiku la Qiyâma, ndithu ndiononga mbumba yake (yonse) kupatula ochepa basi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek