×

Nena, “Ngati angelo akadakhala pa dziko lapansi, namayenda mwamtendere, ndithudi, Ife tikadatumiza 17:95 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:95) ayat 95 in Chichewa

17:95 Surah Al-Isra’ ayat 95 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 95 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قُل لَّوۡ كَانَ فِي ٱلۡأَرۡضِ مَلَٰٓئِكَةٞ يَمۡشُونَ مُطۡمَئِنِّينَ لَنَزَّلۡنَا عَلَيۡهِم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ مَلَكٗا رَّسُولٗا ﴾
[الإسرَاء: 95]

Nena, “Ngati angelo akadakhala pa dziko lapansi, namayenda mwamtendere, ndithudi, Ife tikadatumiza kwa iwo mngelo kuchoka kumwamba ngati Mtumwi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لو كان في الأرض ملائكة يمشون مطمئنين لنـزلنا عليهم من السماء, باللغة نيانجا

﴿قل لو كان في الأرض ملائكة يمشون مطمئنين لنـزلنا عليهم من السماء﴾ [الإسرَاء: 95]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Padziko pakadakhala angelo omayendayenda ndi okhazikika (m’malo awo ndi m’nyumba zawo), tikadawatsitsira m’ngelo monga mtumiki kuchokera kumwamba.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek