×

Pamene inu muwapewa iwo pamodzi ndi zimene iwo akupembedza osati Mulungu, thawirani 18:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:16) ayat 16 in Chichewa

18:16 Surah Al-Kahf ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 16 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿وَإِذِ ٱعۡتَزَلۡتُمُوهُمۡ وَمَا يَعۡبُدُونَ إِلَّا ٱللَّهَ فَأۡوُۥٓاْ إِلَى ٱلۡكَهۡفِ يَنشُرۡ لَكُمۡ رَبُّكُم مِّن رَّحۡمَتِهِۦ وَيُهَيِّئۡ لَكُم مِّنۡ أَمۡرِكُم مِّرۡفَقٗا ﴾
[الكَهف: 16]

Pamene inu muwapewa iwo pamodzi ndi zimene iwo akupembedza osati Mulungu, thawirani kuphanga kuti mukapeze mpumulo. Ambuye wanu adzakutambasulirani chisoni chake ndi kukukonzerani njira yoti zinthu zikupepukireni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ اعتزلتموهم وما يعبدون إلا الله فأووا إلى الكهف ينشر لكم ربكم, باللغة نيانجا

﴿وإذ اعتزلتموهم وما يعبدون إلا الله فأووا إلى الكهف ينشر لكم ربكم﴾ [الكَهف: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“(Adauzana pakati pawo): “Ndipo ngati muwapatuka ndizimene akuzipembedza kusiya Allah, thawirani kuphanga; Mbuye wanu akutambasulirani chifundo Chake ndikukufewetserani zinthu zanu zonse.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek