Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 38 - الكَهف - Page - Juz 15
﴿لَّٰكِنَّا۠ هُوَ ٱللَّهُ رَبِّي وَلَآ أُشۡرِكُ بِرَبِّيٓ أَحَدٗا ﴾
[الكَهف: 38]
﴿لكنا هو الله ربي ولا أشرك بربي أحدا﴾ [الكَهف: 38]
Khaled Ibrahim Betala ““Koma ine ndikukhulupirira kuti Iye ndi Mulungu Mbuye wanga, ndipo sindiphatikiza aliyense ndi Mbuye wanga.” |