×

Ndithudi! Ife tazipanga zimene zili m’dziko lapansi kukhala zokongola ndi cholinga chakuti 18:7 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:7) ayat 7 in Chichewa

18:7 Surah Al-Kahf ayat 7 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 7 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿إِنَّا جَعَلۡنَا مَا عَلَى ٱلۡأَرۡضِ زِينَةٗ لَّهَا لِنَبۡلُوَهُمۡ أَيُّهُمۡ أَحۡسَنُ عَمَلٗا ﴾
[الكَهف: 7]

Ndithudi! Ife tazipanga zimene zili m’dziko lapansi kukhala zokongola ndi cholinga chakuti tiwayese kuti ndani mwa iwo ali wochita zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنا جعلنا ما على الأرض زينة لها لنبلوهم أيهم أحسن عملا, باللغة نيانجا

﴿إنا جعلنا ما على الأرض زينة لها لنبلوهم أيهم أحسن عملا﴾ [الكَهف: 7]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Ife tazichita zomwe zili pamwamba pa nthaka kukhala zokometsera nthakayo, ndikuti (mwa izo) tiwayese mayeso kuti (ndani) mwa iwo ali wochita zabwino kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek