Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 8 - الكَهف - Page - Juz 15
﴿وَإِنَّا لَجَٰعِلُونَ مَا عَلَيۡهَا صَعِيدٗا جُرُزًا ﴾
[الكَهف: 8]
﴿وإنا لجاعلون ما عليها صعيدا جرزا﴾ [الكَهف: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu Ife ndi Amene tidzazichita zomwe zili pamenepo kukhala monga nthaka yoguga (yopanda mmera) |