×

Ndipo onse adapitirizabe ulendo wawo mpaka pamene adakumana ndi mnyamata wina amene 18:74 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:74) ayat 74 in Chichewa

18:74 Surah Al-Kahf ayat 74 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 74 - الكَهف - Page - Juz 15

﴿فَٱنطَلَقَا حَتَّىٰٓ إِذَا لَقِيَا غُلَٰمٗا فَقَتَلَهُۥ قَالَ أَقَتَلۡتَ نَفۡسٗا زَكِيَّةَۢ بِغَيۡرِ نَفۡسٖ لَّقَدۡ جِئۡتَ شَيۡـٔٗا نُّكۡرٗا ﴾
[الكَهف: 74]

Ndipo onse adapitirizabe ulendo wawo mpaka pamene adakumana ndi mnyamata wina amene iye adamupha. Ndipo Mose adati, “Kodi iwe wapha munthu wosalakwa amene sadaphepo wina aliyense? Ndithudi iwe wachita chinthu choipa kwambiri.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فانطلقا حتى إذا لقيا غلاما فقتله قال أقتلت نفسا زكية بغير نفس, باللغة نيانجا

﴿فانطلقا حتى إذا لقيا غلاما فقتله قال أقتلت نفسا زكية بغير نفس﴾ [الكَهف: 74]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adanyamuka; mpaka pomwe adakumana ndi mnyamata wochepa, ndipo (mneneri Khidir) adamupha. Mûsa adati: “Ha! Wapha munthu wopanda cholakwa, pomwe sadaphe munthu mnzake? Ndithu wachita chinthu choipitsitsa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek