×

Chikakhala chombo chija eni ake adali anthu osauka amene amagwira ntchito pa 18:79 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Kahf ⮕ (18:79) ayat 79 in Chichewa

18:79 Surah Al-Kahf ayat 79 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Kahf ayat 79 - الكَهف - Page - Juz 16

﴿أَمَّا ٱلسَّفِينَةُ فَكَانَتۡ لِمَسَٰكِينَ يَعۡمَلُونَ فِي ٱلۡبَحۡرِ فَأَرَدتُّ أَنۡ أَعِيبَهَا وَكَانَ وَرَآءَهُم مَّلِكٞ يَأۡخُذُ كُلَّ سَفِينَةٍ غَصۡبٗا ﴾
[الكَهف: 79]

Chikakhala chombo chija eni ake adali anthu osauka amene amagwira ntchito pa nyanja. Ndipo ine ndinafuna kuti ndichiononge chifukwa kutsogolo kwawo kudali mfumu yomwe imalanda chombo chilichonse mwamphamvu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أما السفينة فكانت لمساكين يعملون في البحر فأردت أن أعيبها وكان وراءهم, باللغة نيانجا

﴿أما السفينة فكانت لمساكين يعملون في البحر فأردت أن أعيبها وكان وراءهم﴾ [الكَهف: 79]

Khaled Ibrahim Betala
““Tsopano chombo chija, chidali cha masikini ogwira ntchito pa nyanja, ndipo ndidafuna kuchiononga (mwadala) chifukwa patsogolo pawo padali mfumu yomwe imatenga chombo chilichonse (chabwino) molanda.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek