×

Ndipo ululu wa kubereka udamubwerera pamene adali patsinde pa mtengo wa tende 19:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:23) ayat 23 in Chichewa

19:23 Surah Maryam ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 23 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿فَأَجَآءَهَا ٱلۡمَخَاضُ إِلَىٰ جِذۡعِ ٱلنَّخۡلَةِ قَالَتۡ يَٰلَيۡتَنِي مِتُّ قَبۡلَ هَٰذَا وَكُنتُ نَسۡيٗا مَّنسِيّٗا ﴾
[مَريَم: 23]

Ndipo ululu wa kubereka udamubwerera pamene adali patsinde pa mtengo wa tende ndipo adalira nati, “Kalanga ine, bola ndikadangofa zisanachitike izi chifukwa ndikadakhala woiwalidwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأجاءها المخاض إلى جذع النخلة قالت ياليتني مت قبل هذا وكنت نسيا, باللغة نيانجا

﴿فأجاءها المخاض إلى جذع النخلة قالت ياليتني مت قبل هذا وكنت نسيا﴾ [مَريَم: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo matenda auchembere (atakwana), adampititsa ku thunthu la mtengo wa kanjedza (wouma kuti awutsamire pomubala mwanayo) adati: “Kalanga ine! Ndiponi ndikadafa izi zisanachitike ndikadakhala nditaiwalidwa ndithu.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek