Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 4 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿قَالَ رَبِّ إِنِّي وَهَنَ ٱلۡعَظۡمُ مِنِّي وَٱشۡتَعَلَ ٱلرَّأۡسُ شَيۡبٗا وَلَمۡ أَكُنۢ بِدُعَآئِكَ رَبِّ شَقِيّٗا ﴾
[مَريَم: 4]
﴿قال رب إني وهن العظم مني واشتعل الرأس شيبا ولم أكن بدعائك﴾ [مَريَم: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Adati: “E Mbuye wanga! Ndithu mafupa anga afooka, ndipo mutu wanga wayaka (ukung’anima) ndi imvi; sindidali watsoka pokupemphani Mbuye wanga (koma nthawi iliyonse ndikakupemphani mumandivomereza) |