Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 47 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿قَالَ سَلَٰمٌ عَلَيۡكَۖ سَأَسۡتَغۡفِرُ لَكَ رَبِّيٓۖ إِنَّهُۥ كَانَ بِي حَفِيّٗا ﴾
[مَريَم: 47]
﴿قال سلام عليك سأستغفر لك ربي إنه كان بي حفيا﴾ [مَريَم: 47]
Khaled Ibrahim Betala “(Ibrahim) adati: “Mtendere ukhale pa inu! Ndikupempherani chikhululuko kwa Mbuye wanga (ngakhale mwandipirikitsa). Ndithu iye amandichitira chisoni kwambiri.” |