×

Koma mibadwo ya anthu imene inadza iwo atachoka idanyoza mapemphero ndi kutsatira 19:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:59) ayat 59 in Chichewa

19:59 Surah Maryam ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 59 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿۞ فَخَلَفَ مِنۢ بَعۡدِهِمۡ خَلۡفٌ أَضَاعُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَٱتَّبَعُواْ ٱلشَّهَوَٰتِۖ فَسَوۡفَ يَلۡقَوۡنَ غَيًّا ﴾
[مَريَم: 59]

Koma mibadwo ya anthu imene inadza iwo atachoka idanyoza mapemphero ndi kutsatira zilakolako zawo. Ndithudi awa adzakumana ndi mavuto

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فخلف من بعدهم خلف أضاعوا الصلاة واتبعوا الشهوات فسوف يلقون غيا, باللغة نيانجا

﴿فخلف من بعدهم خلف أضاعوا الصلاة واتبعوا الشهوات فسوف يلقون غيا﴾ [مَريَم: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma pambuyo pa iwo padadza anthu oipa. Adasokoneza Swala (adasiya kupemphera) natsatira zilakolako zoipa; choncho adzakumana ndi chilango choipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek