×

Zakariya adati, “Ambuye! Kodi ine ndingakhale ndi mwana wamwamuna bwanji, pamene mkazi 19:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:8) ayat 8 in Chichewa

19:8 Surah Maryam ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 8 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿قَالَ رَبِّ أَنَّىٰ يَكُونُ لِي غُلَٰمٞ وَكَانَتِ ٱمۡرَأَتِي عَاقِرٗا وَقَدۡ بَلَغۡتُ مِنَ ٱلۡكِبَرِ عِتِيّٗا ﴾
[مَريَم: 8]

Zakariya adati, “Ambuye! Kodi ine ndingakhale ndi mwana wamwamuna bwanji, pamene mkazi wanga ndi chumba ndipo ine ndine wokalamba?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال رب أنى يكون لي غلام وكانت امرأتي عاقرا وقد بلغت من, باللغة نيانجا

﴿قال رب أنى يكون لي غلام وكانت امرأتي عاقرا وقد بلغت من﴾ [مَريَم: 8]

Khaled Ibrahim Betala
“(Zakariya) adati: “Mbuye wanga! Ndingapeze bwanji mwana pomwe mkazi wanga ndi nkhalamba yosabereka ndipo ine ndafikanso pa ukulu wopyola muyeso?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek