Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 86 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿وَنَسُوقُ ٱلۡمُجۡرِمِينَ إِلَىٰ جَهَنَّمَ وِرۡدٗا ﴾
[مَريَم: 86]
﴿ونسوق المجرمين إلى جهنم وردا﴾ [مَريَم: 86]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo oipa tidzawakusa kunka nawo ku Moto ali ndi ludzu lalikulu monga momwe ziweto zimathamangira kupita kumadzi zikakhala ndi ludzu lalikulu |