Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 85 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿يَوۡمَ نَحۡشُرُ ٱلۡمُتَّقِينَ إِلَى ٱلرَّحۡمَٰنِ وَفۡدٗا ﴾ 
[مَريَم: 85]
﴿يوم نحشر المتقين إلى الرحمن وفدا﴾ [مَريَم: 85]
| Khaled Ibrahim Betala “(Kumbukira iwe Mtumiki) tsiku lomwe tidzawasonkhanitsa oopa (Allah) kunka nawo kwa Mwini chifundo Chambiri ali m’magulumagulu monga nthumwi (Zake kuti apatsidwe ulemu) |