Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 204 - البَقَرَة - Page - Juz 2
﴿وَمِنَ ٱلنَّاسِ مَن يُعۡجِبُكَ قَوۡلُهُۥ فِي ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَا وَيُشۡهِدُ ٱللَّهَ عَلَىٰ مَا فِي قَلۡبِهِۦ وَهُوَ أَلَدُّ ٱلۡخِصَامِ ﴾
[البَقَرَة: 204]
﴿ومن الناس من يعجبك قوله في الحياة الدنيا ويشهد الله على ما﴾ [البَقَرَة: 204]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo mwa anthu alipo amene zoyankhula zake zikukondweretsa (iwe) pano pa dziko la pansi, (koma tsiku lachimaliziro kuipa kwake kudzadziwika). Ndipo iye akutsimikizira Allah kuti akhale mboni pa zomwe zili mu mtima mwake pomwe iye ndi wa makani kwambiri |