×

oh inu anthu okhulupirira! Perekani chopereka cha ulere kuchokera ku chuma chimene 2:267 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:267) ayat 267 in Chichewa

2:267 Surah Al-Baqarah ayat 267 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 267 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُوٓاْ أَنفِقُواْ مِن طَيِّبَٰتِ مَا كَسَبۡتُمۡ وَمِمَّآ أَخۡرَجۡنَا لَكُم مِّنَ ٱلۡأَرۡضِۖ وَلَا تَيَمَّمُواْ ٱلۡخَبِيثَ مِنۡهُ تُنفِقُونَ وَلَسۡتُم بِـَٔاخِذِيهِ إِلَّآ أَن تُغۡمِضُواْ فِيهِۚ وَٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّ ٱللَّهَ غَنِيٌّ حَمِيدٌ ﴾
[البَقَرَة: 267]

oh inu anthu okhulupirira! Perekani chopereka cha ulere kuchokera ku chuma chimene mwachipeza mwa chilungamo ndiponso icho chimene Ife takupatsani kuchokera ku nthaka ndipo musamasankha kupereka chinthu chimene inu simungathe kulandira pokhapokha mutatseka maso anu. Ndipo dziwani kuti Mulungu ndi wolemera ndiponso woyenera kulemekezedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا أنفقوا من طيبات ما كسبتم ومما أخرجنا لكم من, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا أنفقوا من طيبات ما كسبتم ومما أخرجنا لكم من﴾ [البَقَرَة: 267]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu amene mwakhulupirira! Perekani zabwino zochokera m’zimene mwapeza ndi zimene takutulutsirani m’nthaka, ndipo musalinge kupereka choipa chomwe inu simukadachilandira (ngati akanakupatsani) pokhapokha mochitsinzinira. (Nanga Allah ndiye alandire choipacho)? Ndipo dziwani kuti Allah Ngolemera (ndiponso) Ngotamandidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek