×

Ndipo liopeni tsiku limene mudzabwerera kwa Mulungu. Ndipo mzimu uliwonse udzalipidwa molingana 2:281 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:281) ayat 281 in Chichewa

2:281 Surah Al-Baqarah ayat 281 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 281 - البَقَرَة - Page - Juz 3

﴿وَٱتَّقُواْ يَوۡمٗا تُرۡجَعُونَ فِيهِ إِلَى ٱللَّهِۖ ثُمَّ تُوَفَّىٰ كُلُّ نَفۡسٖ مَّا كَسَبَتۡ وَهُمۡ لَا يُظۡلَمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 281]

Ndipo liopeni tsiku limene mudzabwerera kwa Mulungu. Ndipo mzimu uliwonse udzalipidwa molingana ndi ntchito zake, ndipo palibe amene adzaponderezedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واتقوا يوما ترجعون فيه إلى الله ثم توفى كل نفس ما كسبت, باللغة نيانجا

﴿واتقوا يوما ترجعون فيه إلى الله ثم توفى كل نفس ما كسبت﴾ [البَقَرَة: 281]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo liopeni tsiku lomwe inu mudzabwezedwa kwa Allah. Ndipo kenako munthu aliyense adzalipidwa mokwanira pa zonse zimene adachita (ndi manja ake), ndipo iwo sadzaponderezedwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek