Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 280 - البَقَرَة - Page - Juz 3
﴿وَإِن كَانَ ذُو عُسۡرَةٖ فَنَظِرَةٌ إِلَىٰ مَيۡسَرَةٖۚ وَأَن تَصَدَّقُواْ خَيۡرٞ لَّكُمۡ إِن كُنتُمۡ تَعۡلَمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 280]
﴿وإن كان ذو عسرة فنظرة إلى ميسرة وأن تصدقوا خير لكم إن﴾ [البَقَرَة: 280]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati wokongola ali ndi mavuto, choncho (wokongoza) amdikire mpaka apeze bwino. Koma ngati inu (okongoza mungakhululuke pakusiya kuitanitsa ngongole) muisintha kuti ikhale sadaka, ndibwino kwa inu ngati mukudziwa (zimenezo) |