×

Ndipo khulupirirani mu zimene ndatumiza zimene zichitira umboni chivumbulutso chimene muli nacho, 2:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:41) ayat 41 in Chichewa

2:41 Surah Al-Baqarah ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 41 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَءَامِنُواْ بِمَآ أَنزَلۡتُ مُصَدِّقٗا لِّمَا مَعَكُمۡ وَلَا تَكُونُوٓاْ أَوَّلَ كَافِرِۭ بِهِۦۖ وَلَا تَشۡتَرُواْ بِـَٔايَٰتِي ثَمَنٗا قَلِيلٗا وَإِيَّٰيَ فَٱتَّقُونِ ﴾
[البَقَرَة: 41]

Ndipo khulupirirani mu zimene ndatumiza zimene zichitira umboni chivumbulutso chimene muli nacho, kotero inu musakhale anthu oyamba kuzikana, ndipo musagule ndi mau anga kanthu kakang’ono. Ndipo ndiopeni Ine ndekha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وآمنوا بما أنـزلت مصدقا لما معكم ولا تكونوا أول كافر به ولا, باللغة نيانجا

﴿وآمنوا بما أنـزلت مصدقا لما معكم ولا تكونوا أول كافر به ولا﴾ [البَقَرَة: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo khulupirirani zimene ndavumbulutsa, zomwe zikuchitira umboni zimene muli nazo, ndipo musakhale oyamba kuzikana; ndipo musagulitse mawu Anga ndi (zinthu za) mtengo wochepa. Ndipo Ine Ndekha ndiopeni
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek