×

Kodi inu muli kuganiza kuti iwo adzakukhulupirirani ngakh ale kuti gulu lina 2:75 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:75) ayat 75 in Chichewa

2:75 Surah Al-Baqarah ayat 75 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 75 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿۞ أَفَتَطۡمَعُونَ أَن يُؤۡمِنُواْ لَكُمۡ وَقَدۡ كَانَ فَرِيقٞ مِّنۡهُمۡ يَسۡمَعُونَ كَلَٰمَ ٱللَّهِ ثُمَّ يُحَرِّفُونَهُۥ مِنۢ بَعۡدِ مَا عَقَلُوهُ وَهُمۡ يَعۡلَمُونَ ﴾
[البَقَرَة: 75]

Kodi inu muli kuganiza kuti iwo adzakukhulupirirani ngakh ale kuti gulu lina linali kumva mawu a Mulungu ndipo anali kumawasintha pamene iwo ali kuzindikira ndiponso iwo ali kudziwa chimenechi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أفتطمعون أن يؤمنوا لكم وقد كان فريق منهم يسمعون كلام الله ثم, باللغة نيانجا

﴿أفتطمعون أن يؤمنوا لكم وقد كان فريق منهم يسمعون كلام الله ثم﴾ [البَقَرَة: 75]

Khaled Ibrahim Betala
۞ Kodi (inu Asilamu) mukuyembekezera kuti angakukhulupirireni (Ayudawo) pomwe ena a iwo ankamvera mawu a Allah, kenako nkuwasintha pambuyo powazindikira bwinobwino, uku akudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek