×

Nena: “Ngati nyumba zamtsogolo za Mulungu ndi zanu zokha ndipo kuti sizidzapatsidwa 2:94 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:94) ayat 94 in Chichewa

2:94 Surah Al-Baqarah ayat 94 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 94 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿قُلۡ إِن كَانَتۡ لَكُمُ ٱلدَّارُ ٱلۡأٓخِرَةُ عِندَ ٱللَّهِ خَالِصَةٗ مِّن دُونِ ٱلنَّاسِ فَتَمَنَّوُاْ ٱلۡمَوۡتَ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[البَقَرَة: 94]

Nena: “Ngati nyumba zamtsogolo za Mulungu ndi zanu zokha ndipo kuti sizidzapatsidwa kwa anthu ena, lakalakani imfa ngati zimene munena ndi zoona.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل إن كانت لكم الدار الآخرة عند الله خالصة من دون الناس, باللغة نيانجا

﴿قل إن كانت لكم الدار الآخرة عند الله خالصة من دون الناس﴾ [البَقَرَة: 94]

Khaled Ibrahim Betala
“Auze (Ayudawo): “Ngati nyumba yomaliza kwa Allah njanu nokha, osati anthu ena (monga momwe mukunenera), ilakalakeni imfa ngati mukunenadi zoona.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek