×

Ndithudi iwe udzawapeza kuti iwo amakonda kwambiri moyo uno kuposa aja amene 2:96 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:96) ayat 96 in Chichewa

2:96 Surah Al-Baqarah ayat 96 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 96 - البَقَرَة - Page - Juz 1

﴿وَلَتَجِدَنَّهُمۡ أَحۡرَصَ ٱلنَّاسِ عَلَىٰ حَيَوٰةٖ وَمِنَ ٱلَّذِينَ أَشۡرَكُواْۚ يَوَدُّ أَحَدُهُمۡ لَوۡ يُعَمَّرُ أَلۡفَ سَنَةٖ وَمَا هُوَ بِمُزَحۡزِحِهِۦ مِنَ ٱلۡعَذَابِ أَن يُعَمَّرَۗ وَٱللَّهُ بَصِيرُۢ بِمَا يَعۡمَلُونَ ﴾
[البَقَرَة: 96]

Ndithudi iwe udzawapeza kuti iwo amakonda kwambiri moyo uno kuposa aja amene amaphatikiza Mulungu ndi zinthu zina ndipo sakhulupirira kuti kuli kuuka kwa akufa. Aliyense wa iwo akadakondwera ngati akadapatsidwa moyo wokwana zaka chikwi chimodzi. Komabe ngakhale atawonjezeredwa moyo wautali, siungamuchotsere chilango. Ndipo Mulungu ali kuona zonse zimene ali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولتجدنهم أحرص الناس على حياة ومن الذين أشركوا يود أحدهم لو يعمر, باللغة نيانجا

﴿ولتجدنهم أحرص الناس على حياة ومن الذين أشركوا يود أحدهم لو يعمر﴾ [البَقَرَة: 96]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo muwapeza (Ayuda) kuti ngokondetsetsa kukhala ndi moyo wautali kuposa anthu ena, kuposanso anthu amene akuphatikiza (Allah ndi mafano). Aliyense wa iwo amafuna atapatsidwa moyo wokwana zaka chikwi chimodzi. Pomwe kupatsidwa kwake moyo wautali sikungamuike kutali ndi chilango. Ndipo Allah akuona zonse zimene akuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek