Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 103 - طه - Page - Juz 16
﴿يَتَخَٰفَتُونَ بَيۡنَهُمۡ إِن لَّبِثۡتُمۡ إِلَّا عَشۡرٗا ﴾
[طه: 103]
﴿يتخافتون بينهم إن لبثتم إلا عشرا﴾ [طه: 103]
Khaled Ibrahim Betala “Adzanong’onezana pakati pawo (ponena kuti): “Simudakhalitse pa dziko lapansi koma masiku khumi okha basi.” |