Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 21 - الأنبيَاء - Page - Juz 17
﴿أَمِ ٱتَّخَذُوٓاْ ءَالِهَةٗ مِّنَ ٱلۡأَرۡضِ هُمۡ يُنشِرُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 21]
﴿أم اتخذوا آلهة من الأرض هم ينشرون﴾ [الأنبيَاء: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Kapena adzipangira milungu yochokera m’nthaka youkitsa akufa, (kotero kuti aichita kukhala milungu yawo mmalo mwa Allah) |