×

Kukadakhala milungu ina kumeneko yoonjezera pa Mulungu weniweni, ndithudi, konse kukadaonongeka. Alemekezeke 21:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:22) ayat 22 in Chichewa

21:22 Surah Al-Anbiya’ ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 22 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿لَوۡ كَانَ فِيهِمَآ ءَالِهَةٌ إِلَّا ٱللَّهُ لَفَسَدَتَاۚ فَسُبۡحَٰنَ ٱللَّهِ رَبِّ ٱلۡعَرۡشِ عَمَّا يَصِفُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 22]

Kukadakhala milungu ina kumeneko yoonjezera pa Mulungu weniweni, ndithudi, konse kukadaonongeka. Alemekezeke Mulungu, Mwini wa Mpando wa Chifumu, mu zimene akumunenera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لو كان فيهما آلهة إلا الله لفسدتا فسبحان الله رب العرش عما, باللغة نيانجا

﴿لو كان فيهما آلهة إلا الله لفسدتا فسبحان الله رب العرش عما﴾ [الأنبيَاء: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Kukadakhala kuti ilipo m’menemo milungu ina (kuthambo ndi pansi) kupatula Allah, (ziwirizi) zikadawonongeka, wapatukana Allah Mbuye wa Arsh (Mpando Wachifumu) ndi zimene akunena (osakhulupirira)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek