×

Ku mtundu uliwonse, Ife tidakhazikitsa miyambo yachipembedzo kuti azitchula dzina la Mulungu 22:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:34) ayat 34 in Chichewa

22:34 Surah Al-hajj ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 34 - الحج - Page - Juz 17

﴿وَلِكُلِّ أُمَّةٖ جَعَلۡنَا مَنسَكٗا لِّيَذۡكُرُواْ ٱسۡمَ ٱللَّهِ عَلَىٰ مَا رَزَقَهُم مِّنۢ بَهِيمَةِ ٱلۡأَنۡعَٰمِۗ فَإِلَٰهُكُمۡ إِلَٰهٞ وَٰحِدٞ فَلَهُۥٓ أَسۡلِمُواْۗ وَبَشِّرِ ٱلۡمُخۡبِتِينَ ﴾
[الحج: 34]

Ku mtundu uliwonse, Ife tidakhazikitsa miyambo yachipembedzo kuti azitchula dzina la Mulungu pa nyama zimene Iyeadawapatsaiwongatichakudya. Ndipo Mulungu wanu ndi Mulungu mmodzi yekha motero muzigonjera Iye yekha. Auzeni nkhani yabwino anthu onse odzichepetsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولكل أمة جعلنا منسكا ليذكروا اسم الله على ما رزقهم من بهيمة, باللغة نيانجا

﴿ولكل أمة جعلنا منسكا ليذكروا اسم الله على ما رزقهم من بهيمة﴾ [الحج: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mpingo uliwonse tidaupangira malo ozingira nsembe zamapemphero kuti atchule dzina la Allah pa zomwe wawapatsa monga ziweto zamiyendo inayi. Choncho mulungu wanu ndi Mulungu m’modzi Yekha; gonjerani kwa Iye; ndipo odzichepetsa auze nkhani yabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek