Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 9 - الحج - Page - Juz 17
﴿ثَانِيَ عِطۡفِهِۦ لِيُضِلَّ عَن سَبِيلِ ٱللَّهِۖ لَهُۥ فِي ٱلدُّنۡيَا خِزۡيٞۖ وَنُذِيقُهُۥ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ عَذَابَ ٱلۡحَرِيقِ ﴾
[الحج: 9]
﴿ثاني عطفه ليضل عن سبيل الله له في الدنيا خزي ونذيقه يوم﴾ [الحج: 9]
Khaled Ibrahim Betala “(Yemwe) akupinda khosi lake (chifukwa chodzikuza) kuti asokereze (anthu powachotsa) kunjira ya Allah; pa iye pali chilango choyalutsa pa moyo uno, ndipo patsiku la Qiyâma tikamulawitsa chilango cha Moto wotentha |