×

Iwo adzayankha kuti, “Takhala tsiku limodzi kapena mphindi zochepa zokha. Afunseni iwo 23:113 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mu’minun ⮕ (23:113) ayat 113 in Chichewa

23:113 Surah Al-Mu’minun ayat 113 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 113 - المؤمنُون - Page - Juz 18

﴿قَالُواْ لَبِثۡنَا يَوۡمًا أَوۡ بَعۡضَ يَوۡمٖ فَسۡـَٔلِ ٱلۡعَآدِّينَ ﴾
[المؤمنُون: 113]

Iwo adzayankha kuti, “Takhala tsiku limodzi kapena mphindi zochepa zokha. Afunseni iwo amene amasunga chiwerengero.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا لبثنا يوما أو بعض يوم فاسأل العادين, باللغة نيانجا

﴿قالوا لبثنا يوما أو بعض يوم فاسأل العادين﴾ [المؤمنُون: 113]

Khaled Ibrahim Betala
“Adzayankha: “Tidakhala tsiku limodzi kapena gawo la tsiku; afunse owerengera.” (Adzatero poyerekeza ndi kutalika kwa moyo wamasautso ku Moto)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek