Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 52 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿وَإِنَّ هَٰذِهِۦٓ أُمَّتُكُمۡ أُمَّةٗ وَٰحِدَةٗ وَأَنَا۠ رَبُّكُمۡ فَٱتَّقُونِ ﴾
[المؤمنُون: 52]
﴿وإن هذه أمتكم أمة واحدة وأنا ربكم فاتقون﴾ [المؤمنُون: 52]
Khaled Ibrahim Betala “(Tidauza mibadwo yawo): “Ndithu mpingo wanuwu ndi mpingo umodzi, ndipo Ine Ndine Mbuye wanu; choncho ndiopeni.” |